Quran with Chichewa translation - Surah Al-Insan ayat 7 - الإنسَان - Page - Juz 29
﴿يُوفُونَ بِٱلنَّذۡرِ وَيَخَافُونَ يَوۡمٗا كَانَ شَرُّهُۥ مُسۡتَطِيرٗا ﴾
[الإنسَان: 7]
﴿يوفون بالنذر ويخافون يوما كان شره مستطيرا﴾ [الإنسَان: 7]
Khaled Ibrahim Betala “(Amene) akukwaniritsa zimene adalonjeza (okha kwa Allah), ndiponso akuopa tsiku (lalikulu) limene zoipa zake zidzakhala zofalikira ponseponse |