Quran with Chichewa translation - Surah An-Naba’ ayat 39 - النَّبَإ - Page - Juz 30
﴿ذَٰلِكَ ٱلۡيَوۡمُ ٱلۡحَقُّۖ فَمَن شَآءَ ٱتَّخَذَ إِلَىٰ رَبِّهِۦ مَـَٔابًا ﴾
[النَّبَإ: 39]
﴿ذلك اليوم الحق فمن شاء اتخذ إلى ربه مآبا﴾ [النَّبَإ: 39]
Khaled Ibrahim Betala “Limenelo ndi tsiku loona, (lopanda chikaiko); choncho amene akufuna adzipezere malo (njira yonkera) kwa Mbuye wake. (Pomugonjera Iye pa moyo uno wadziko lapansi) |