Quran with Chichewa translation - Surah An-Nazi‘at ayat 27 - النَّازعَات - Page - Juz 30
﴿ءَأَنتُمۡ أَشَدُّ خَلۡقًا أَمِ ٱلسَّمَآءُۚ بَنَىٰهَا ﴾ 
[النَّازعَات: 27]
﴿أأنتم أشد خلقا أم السماء بناها﴾ [النَّازعَات: 27]
| Khaled Ibrahim Betala “Kodi kulengedwa kwanu, (inu osakhulupirira kuti muuke) nkovuta kapena thambo limene adalimanga (posonkhanitsa mbali zake zosiyanasiyana ndikukhala chinthu chimodzi)  |