Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 26 - الأنفَال - Page - Juz 9
﴿وَٱذۡكُرُوٓاْ إِذۡ أَنتُمۡ قَلِيلٞ مُّسۡتَضۡعَفُونَ فِي ٱلۡأَرۡضِ تَخَافُونَ أَن يَتَخَطَّفَكُمُ ٱلنَّاسُ فَـَٔاوَىٰكُمۡ وَأَيَّدَكُم بِنَصۡرِهِۦ وَرَزَقَكُم مِّنَ ٱلطَّيِّبَٰتِ لَعَلَّكُمۡ تَشۡكُرُونَ ﴾
[الأنفَال: 26]
﴿واذكروا إذ أنتم قليل مستضعفون في الأرض تخافون أن يتخطفكم الناس فآواكم﴾ [الأنفَال: 26]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo kumbukirani (inu Asilamu) pamene mudali owerengeka, ochepa, onyozeka m’dziko. Mumakhala moopa anthu kuti angakufwambeni, koma anakupatsani pamalo pabwino pokhala, nakulimbikitsani ndi chipulumutso Chake, nakuninkhani zinthu zabwino kuti muyamike (Allah) |