×

Ndipo pamene chivumbulutso chathu chilakatulidwa kwa iwo, iwo amati: “Ife tamva kale 8:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:31) ayat 31 in Chichewa

8:31 Surah Al-Anfal ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 31 - الأنفَال - Page - Juz 9

﴿وَإِذَا تُتۡلَىٰ عَلَيۡهِمۡ ءَايَٰتُنَا قَالُواْ قَدۡ سَمِعۡنَا لَوۡ نَشَآءُ لَقُلۡنَا مِثۡلَ هَٰذَآ إِنۡ هَٰذَآ إِلَّآ أَسَٰطِيرُ ٱلۡأَوَّلِينَ ﴾
[الأنفَال: 31]

Ndipo pamene chivumbulutso chathu chilakatulidwa kwa iwo, iwo amati: “Ife tamva kale ndipo ngati ife tikanafuna, tikhoza kunena cholingana nacho. Izi si zina koma nkhani zopanda pake za anthu akale.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا تتلى عليهم آياتنا قالوا قد سمعنا لو نشاء لقلنا مثل هذا, باللغة نيانجا

﴿وإذا تتلى عليهم آياتنا قالوا قد سمعنا لو نشاء لقلنا مثل هذا﴾ [الأنفَال: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (Aquraish) zikawerengedwa Ayah (ndime) Zathu kwa iwo amanena: “Tidazimva (izi kale). Tikadafuna tikadanena zonga izi. Izi sikanthu koma ndinthano za anthu akale.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek