×

Kodi Mulungu asawalange iwo pamene iwo akhala ali kuletsa ena kuti alowe 8:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:34) ayat 34 in Chichewa

8:34 Surah Al-Anfal ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 34 - الأنفَال - Page - Juz 9

﴿وَمَا لَهُمۡ أَلَّا يُعَذِّبَهُمُ ٱللَّهُ وَهُمۡ يَصُدُّونَ عَنِ ٱلۡمَسۡجِدِ ٱلۡحَرَامِ وَمَا كَانُوٓاْ أَوۡلِيَآءَهُۥٓۚ إِنۡ أَوۡلِيَآؤُهُۥٓ إِلَّا ٱلۡمُتَّقُونَ وَلَٰكِنَّ أَكۡثَرَهُمۡ لَا يَعۡلَمُونَ ﴾
[الأنفَال: 34]

Kodi Mulungu asawalange iwo pamene iwo akhala ali kuletsa ena kuti alowe mu Mzikiti Wolemekezeka ngakhale kuti iwo alibe udindo woteteza Mzikitiwo? Palibe outeteza kupatula okhawo amene amaopa Mulungu, koma ambiri a iwo sadziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما لهم ألا يعذبهم الله وهم يصدون عن المسجد الحرام وما كانوا, باللغة نيانجا

﴿وما لهم ألا يعذبهم الله وهم يصدون عن المسجد الحرام وما كانوا﴾ [الأنفَال: 34]

Khaled Ibrahim Betala
“(Kodi iwo Aquraish) ali ndi chinthu chanji (chabwino chimene) chingamuletse Allah kuwalanga? Pomwe iwo akuwatsekereza anthu kulowa mu Msikiti Wopatulika. Iwo sanayenere kukhala ouyang’anira (Msikitiwo). Palibe angauyang’anire koma olungama, koma anthu ambiri sadziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek