×

Mapemphero awo mu Mzikiti wolemekezeka sadali china chili chonse koma miluzu ndi 8:35 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:35) ayat 35 in Chichewa

8:35 Surah Al-Anfal ayat 35 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 35 - الأنفَال - Page - Juz 9

﴿وَمَا كَانَ صَلَاتُهُمۡ عِندَ ٱلۡبَيۡتِ إِلَّا مُكَآءٗ وَتَصۡدِيَةٗۚ فَذُوقُواْ ٱلۡعَذَابَ بِمَا كُنتُمۡ تَكۡفُرُونَ ﴾
[الأنفَال: 35]

Mapemphero awo mu Mzikiti wolemekezeka sadali china chili chonse koma miluzu ndi kuomba m’manja basi, motero lawani chilango chifukwa inu simunali kukhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما كان صلاتهم عند البيت إلا مكاء وتصدية فذوقوا العذاب بما كنتم, باللغة نيانجا

﴿وما كان صلاتهم عند البيت إلا مكاء وتصدية فذوقوا العذاب بما كنتم﴾ [الأنفَال: 35]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo mapemphero awo pa nyumba yopatulikayo sadali kanthu, koma kuyimba miluzi ndi kuomba m’manja. Choncho (adzauzidwa): “Lawani chilango chifukwa chakusakhulupirira kwanu.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek