×

Kuti Mulunguasiyanitse pakati pa anthu oipa ndi abwino ndi kuwaika anthu oipa 8:37 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:37) ayat 37 in Chichewa

8:37 Surah Al-Anfal ayat 37 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 37 - الأنفَال - Page - Juz 9

﴿لِيَمِيزَ ٱللَّهُ ٱلۡخَبِيثَ مِنَ ٱلطَّيِّبِ وَيَجۡعَلَ ٱلۡخَبِيثَ بَعۡضَهُۥ عَلَىٰ بَعۡضٖ فَيَرۡكُمَهُۥ جَمِيعٗا فَيَجۡعَلَهُۥ فِي جَهَنَّمَۚ أُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلۡخَٰسِرُونَ ﴾
[الأنفَال: 37]

Kuti Mulunguasiyanitse pakati pa anthu oipa ndi abwino ndi kuwaika anthu oipa wina pamwamba pa mnzake, ndipo adzawaunjika onse pamodzi ndi kuwaponya ku Gahena. Awa! Ndiwo amene ali olephera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ليميز الله الخبيث من الطيب ويجعل الخبيث بعضه على بعض فيركمه جميعا, باللغة نيانجا

﴿ليميز الله الخبيث من الطيب ويجعل الخبيث بعضه على بعض فيركمه جميعا﴾ [الأنفَال: 37]

Khaled Ibrahim Betala
“Kuti Allah alekanitse oipa ndi abwino, ndi kuti awayike ena mwa oipawo pamwamba pa anzawo, potero nkuwaunjika oipawo mulu umodzi, kenako nawaponya ku Jahannam. Iwowa ndi anthu otaika
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek