×

Menyanani nawo mpaka pamene kusakhulupirira ndi kupembedza mafano kutha ndipo chipembedzo cha 8:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:39) ayat 39 in Chichewa

8:39 Surah Al-Anfal ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 39 - الأنفَال - Page - Juz 9

﴿وَقَٰتِلُوهُمۡ حَتَّىٰ لَا تَكُونَ فِتۡنَةٞ وَيَكُونَ ٱلدِّينُ كُلُّهُۥ لِلَّهِۚ فَإِنِ ٱنتَهَوۡاْ فَإِنَّ ٱللَّهَ بِمَا يَعۡمَلُونَ بَصِيرٞ ﴾
[الأنفَال: 39]

Menyanani nawo mpaka pamene kusakhulupirira ndi kupembedza mafano kutha ndipo chipembedzo cha Mulungu chikhazikitsidwa ponseponse koma ngati iwo asiya, ndithudi Mulungu akuona zochita zawo zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقاتلوهم حتى لا تكون فتنة ويكون الدين كله لله فإن انتهوا فإن, باللغة نيانجا

﴿وقاتلوهم حتى لا تكون فتنة ويكون الدين كله لله فإن انتهوا فإن﴾ [الأنفَال: 39]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo menyanani nawo osakhulupirira kufikira shirik itatha ndipo chipembedzo chonse chikhale cha Allah. Ndipo ngati asiya, ndithu Allah Ngoona zomwe akuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek