×

Pamene Mulungu adakuonetsam’malotoakongatigululaling’ono.Akadakhala kuti adakuonetsa iwe kuti ndi gulu lalikulu, ndithudi iwe 8:43 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:43) ayat 43 in Chichewa

8:43 Surah Al-Anfal ayat 43 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 43 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿إِذۡ يُرِيكَهُمُ ٱللَّهُ فِي مَنَامِكَ قَلِيلٗاۖ وَلَوۡ أَرَىٰكَهُمۡ كَثِيرٗا لَّفَشِلۡتُمۡ وَلَتَنَٰزَعۡتُمۡ فِي ٱلۡأَمۡرِ وَلَٰكِنَّ ٱللَّهَ سَلَّمَۚ إِنَّهُۥ عَلِيمُۢ بِذَاتِ ٱلصُّدُورِ ﴾
[الأنفَال: 43]

Pamene Mulungu adakuonetsam’malotoakongatigululaling’ono.Akadakhala kuti adakuonetsa iwe kuti ndi gulu lalikulu, ndithudi iwe ukadagwa mphwayi ndipo ukadavutika popereka malamulo. Koma Mulungu adakupulumutsa. Ndithudi Iye amadziwa zinthu zonse zimene zili m’maganizo mwanu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إذ يريكهم الله في منامك قليلا ولو أراكهم كثيرا لفشلتم ولتنازعتم في, باللغة نيانجا

﴿إذ يريكهم الله في منامك قليلا ولو أراكهم كثيرا لفشلتم ولتنازعتم في﴾ [الأنفَال: 43]

Khaled Ibrahim Betala
“(Kumbukira) pamene Allah adakuonetsa iwo ku maloto kwako kuti ngochepa (pachiwerengero chawo potero udalimba mtima za kukumana nawo), akanakuonetsa iwo kuti ngambiri pa chiwerengero chawo; inu (Asilamu) mukadalephera (mukanataya mtima) ndipo mukanakangana pa chinthucho. (Ena akanafuna kumenyana nawo pamene ena akanakana), koma Allah anakutetezani (ku zimenezo). Ndithu Iye Ngodziwa kwambiri za m’mitima
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek