×

Ndi pamene Satana adakometsa ntchito zawo zopusa nati, “Palibe munthu wina aliyense 8:48 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:48) ayat 48 in Chichewa

8:48 Surah Al-Anfal ayat 48 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 48 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿وَإِذۡ زَيَّنَ لَهُمُ ٱلشَّيۡطَٰنُ أَعۡمَٰلَهُمۡ وَقَالَ لَا غَالِبَ لَكُمُ ٱلۡيَوۡمَ مِنَ ٱلنَّاسِ وَإِنِّي جَارٞ لَّكُمۡۖ فَلَمَّا تَرَآءَتِ ٱلۡفِئَتَانِ نَكَصَ عَلَىٰ عَقِبَيۡهِ وَقَالَ إِنِّي بَرِيٓءٞ مِّنكُمۡ إِنِّيٓ أَرَىٰ مَا لَا تَرَوۡنَ إِنِّيٓ أَخَافُ ٱللَّهَۚ وَٱللَّهُ شَدِيدُ ٱلۡعِقَابِ ﴾
[الأنفَال: 48]

Ndi pamene Satana adakometsa ntchito zawo zopusa nati, “Palibe munthu wina aliyense amene adzakugonjetsani inu lero, ndithudi ine ndidzakhala pafupi kukuthandizani inu.” Koma pamene magulu awiri a nkhondo adakumana, iye adathawa ndipo anati: “Ndithudi ine ndilibe nanu ntchito. Ndithudi ine ndaona zimene inu simungathe kuziona. Ndithudi ine ndiopa Mulungu chifukwa chilango chake ndi choopsya.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذ زين لهم الشيطان أعمالهم وقال لا غالب لكم اليوم من الناس, باللغة نيانجا

﴿وإذ زين لهم الشيطان أعمالهم وقال لا غالب لكم اليوم من الناس﴾ [الأنفَال: 48]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (kumbukira) pamene satana adawakometsera zochita zawo zoipa (aja osakhulupirira) nati: “Lero palibe aliyense mwa anthu amene angakugonjetseni, ndipo ine ndine mtetezi wanu.” Koma pamene magulu awiri ankhondo anaonana (anakumana pamaso ndi pamaso) satana anabwerera pambuyo (kuthawa) nati: “Ine ndikudzipatula mwa inu. Ndithu ine ndikuona zimene inu simukuziona. Ndithu ine ndikuopa Allah.” Ndipo Allah Ngwaukali polanga
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek