Quran with Chichewa translation - Surah Al-InfiTar ayat 19 - الانفِطَار - Page - Juz 30
﴿يَوۡمَ لَا تَمۡلِكُ نَفۡسٞ لِّنَفۡسٖ شَيۡـٔٗاۖ وَٱلۡأَمۡرُ يَوۡمَئِذٖ لِّلَّهِ ﴾
[الانفِطَار: 19]
﴿يوم لا تملك نفس لنفس شيئا والأمر يومئذ لله﴾ [الانفِطَار: 19]
Khaled Ibrahim Betala “Limeneli ndi tsiku limene mzimu uliwonse sudzakhala ndi mphamvu (yodzetsa mtendere kapena yochotsa chovuta) pa mzimu wina. Ndipo lamulo pa tsiku limeneli ndi la Allah yekha |