Quran with Chichewa translation - Surah Al-InfiTar ayat 5 - الانفِطَار - Page - Juz 30
﴿عَلِمَتۡ نَفۡسٞ مَّا قَدَّمَتۡ وَأَخَّرَتۡ ﴾
[الانفِطَار: 5]
﴿علمت نفس ما قدمت وأخرت﴾ [الانفِطَار: 5]
Khaled Ibrahim Betala “(Panthawiyo) mzimu uliwonse udzadziwa zimene udatsogoza (zabwino ndi zoipa) ndi zimene udasiya m’mbuyo |