Quran with Chichewa translation - Surah Al-Buruj ayat 8 - البُرُوج - Page - Juz 30
﴿وَمَا نَقَمُواْ مِنۡهُمۡ إِلَّآ أَن يُؤۡمِنُواْ بِٱللَّهِ ٱلۡعَزِيزِ ٱلۡحَمِيدِ ﴾
[البُرُوج: 8]
﴿وما نقموا منهم إلا أن يؤمنوا بالله العزيز الحميد﴾ [البُرُوج: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Sadaone choipa chilichonse mwa iwo koma chifukwa choti adakhulupirira Allah mwini mphamvu zonse ndiponso mwini kuyamikidwa |