Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 106 - التوبَة - Page - Juz 11
﴿وَءَاخَرُونَ مُرۡجَوۡنَ لِأَمۡرِ ٱللَّهِ إِمَّا يُعَذِّبُهُمۡ وَإِمَّا يَتُوبُ عَلَيۡهِمۡۗ وَٱللَّهُ عَلِيمٌ حَكِيمٞ ﴾
[التوبَة: 106]
﴿وآخرون مرجون لأمر الله إما يعذبهم وإما يتوب عليهم والله عليم حكيم﴾ [التوبَة: 106]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo aliponso ena amene (adagwa m’machimo omwe) akuyembekezera lamulo la Allah, (kulapa kwawo sikunavomerezekebe), kapena awalanga kapenanso awavomera kulapa kwawo. Ndipo Allah Ngodziwa (khalidwe lawo ndi zomwe zili m’mitima mwawo), Wanzeru zakuya (pa zonse zomwe akuchita kwa anthu Ake popereka mphoto ndi chilango) |