×

Nena, “Chitani monga momwe mufunira! Mulungu adzaona ntchito zanu ndi Mtumwi wake 9:105 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:105) ayat 105 in Chichewa

9:105 Surah At-Taubah ayat 105 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 105 - التوبَة - Page - Juz 11

﴿وَقُلِ ٱعۡمَلُواْ فَسَيَرَى ٱللَّهُ عَمَلَكُمۡ وَرَسُولُهُۥ وَٱلۡمُؤۡمِنُونَۖ وَسَتُرَدُّونَ إِلَىٰ عَٰلِمِ ٱلۡغَيۡبِ وَٱلشَّهَٰدَةِ فَيُنَبِّئُكُم بِمَا كُنتُمۡ تَعۡمَلُونَ ﴾
[التوبَة: 105]

Nena, “Chitani monga momwe mufunira! Mulungu adzaona ntchito zanu ndi Mtumwi wake ndi anthu okhulupirira. Ndipo inu mudzabwezedwa kwa Iye amene amadziwa zobisika ndi zoonekera. Ndipo Iye adzakuuzani zonse zimene mumachita.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقل اعملوا فسيرى الله عملكم ورسوله والمؤمنون وستردون إلى عالم الغيب والشهادة, باللغة نيانجا

﴿وقل اعملوا فسيرى الله عملكم ورسوله والمؤمنون وستردون إلى عالم الغيب والشهادة﴾ [التوبَة: 105]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo auze: “Gwirani ntchito; Allah ndi Mtumiki Wake ndi okhulupirira aona ntchito yanuyo posachedwa. Ndipo (kenako) mudzabwezedwa kwa Wodziwa zamseri ndi zoonekera poyera. Choncho adzakuuzani zonse (zimene) mudali kuchita.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek