Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 50 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿إِن تُصِبۡكَ حَسَنَةٞ تَسُؤۡهُمۡۖ وَإِن تُصِبۡكَ مُصِيبَةٞ يَقُولُواْ قَدۡ أَخَذۡنَآ أَمۡرَنَا مِن قَبۡلُ وَيَتَوَلَّواْ وَّهُمۡ فَرِحُونَ ﴾
[التوبَة: 50]
﴿إن تصبك حسنة تسؤهم وإن تصبك مصيبة يقولوا قد أخذنا أمرنا من﴾ [التوبَة: 50]
Khaled Ibrahim Betala “Chikakupeza chabwino, (iwe Mtumiki Muhammad (s.a.w) ndi okutsatira) zimawanyansa, ndipo vuto likakupeza amanena: “Tidalingalira zinthu zathu kale. (Nchifukwa chake mavuto atizemba).” Ndipo amatembenuka nkupita uku akukondwa |