×

Nena, “Palibe chimene chingationekere ife kupatula chokhacho chimene Mulungu analamula kuti chidze 9:51 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:51) ayat 51 in Chichewa

9:51 Surah At-Taubah ayat 51 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 51 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿قُل لَّن يُصِيبَنَآ إِلَّا مَا كَتَبَ ٱللَّهُ لَنَا هُوَ مَوۡلَىٰنَاۚ وَعَلَى ٱللَّهِ فَلۡيَتَوَكَّلِ ٱلۡمُؤۡمِنُونَ ﴾
[التوبَة: 51]

Nena, “Palibe chimene chingationekere ife kupatula chokhacho chimene Mulungu analamula kuti chidze pa ife. Iye ndiye Ambuye wathu.” Ndipo mwa Mulungu, anthu onse okhulupirira ayike chikhulupiliro chawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل لن يصيبنا إلا ما كتب الله لنا هو مولانا وعلى الله, باللغة نيانجا

﴿قل لن يصيبنا إلا ما كتب الله لنا هو مولانا وعلى الله﴾ [التوبَة: 51]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Palibe chomwe chitipeze koma chimene Allah watilembera. Iye ndi Mbuye wathu.” Choncho, Asilamu ayadzamire kwa Allah Yekha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek