×

Iwo akadangokhutitsidwa ndi zinthu zimene Mulungu ndi Mtumwi wake adawapatsa, ndi kunena 9:59 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:59) ayat 59 in Chichewa

9:59 Surah At-Taubah ayat 59 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 59 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿وَلَوۡ أَنَّهُمۡ رَضُواْ مَآ ءَاتَىٰهُمُ ٱللَّهُ وَرَسُولُهُۥ وَقَالُواْ حَسۡبُنَا ٱللَّهُ سَيُؤۡتِينَا ٱللَّهُ مِن فَضۡلِهِۦ وَرَسُولُهُۥٓ إِنَّآ إِلَى ٱللَّهِ رَٰغِبُونَ ﴾
[التوبَة: 59]

Iwo akadangokhutitsidwa ndi zinthu zimene Mulungu ndi Mtumwi wake adawapatsa, ndi kunena kuti: “Mulungu ndi okwanira kwa ife. Mulungu adzatipatsa zabwino zake ndiponso Mtumwi wake. Ife timpempha Mulungu.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولو أنهم رضوا ما آتاهم الله ورسوله وقالوا حسبنا الله سيؤتينا الله, باللغة نيانجا

﴿ولو أنهم رضوا ما آتاهم الله ورسوله وقالوا حسبنا الله سيؤتينا الله﴾ [التوبَة: 59]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ngati iwo akadakondwera ndi chimene Allah ndi Mtumiki Wake wawapatsa, nanena: “Allah watikwanira. Posachedwapa Allah ndi Mtumiki Wake atipatsa zabwino Zake. Ndithu ife tikufunitsitsa kwa Allah.” (Ndiye kuti Allah akadawapatsa zambiri)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek