×

Ndipo pakati pawo pali ena amene anachita lonjezo ndi Mulungu ponena kuti: 9:75 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:75) ayat 75 in Chichewa

9:75 Surah At-Taubah ayat 75 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 75 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿۞ وَمِنۡهُم مَّنۡ عَٰهَدَ ٱللَّهَ لَئِنۡ ءَاتَىٰنَا مِن فَضۡلِهِۦ لَنَصَّدَّقَنَّ وَلَنَكُونَنَّ مِنَ ٱلصَّٰلِحِينَ ﴾
[التوبَة: 75]

Ndipo pakati pawo pali ena amene anachita lonjezo ndi Mulungu ponena kuti: “Ngati Iye atipatsa ife chuma, ndithudi, tidzapereka zopereka ndipo tidzakhala m’gulu la anthu abwino.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومنهم من عاهد الله لئن آتانا من فضله لنصدقن ولنكونن من الصالحين, باللغة نيانجا

﴿ومنهم من عاهد الله لئن آتانا من فضله لنصدقن ولنكونن من الصالحين﴾ [التوبَة: 75]

Khaled Ibrahim Betala
“Pakati pawo alipo amene adalonjeza Allah kuti, “Ngati atipatsa zabwino zake (chuma) tidzapereka sadaka ndi kukhala m’gulu la ochita zabwino.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek