×

Iwo amene amaononga mbiri ya anthu okhulupirira amene amapereka mosaumilizidwa ndi iwo 9:79 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:79) ayat 79 in Chichewa

9:79 Surah At-Taubah ayat 79 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 79 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿ٱلَّذِينَ يَلۡمِزُونَ ٱلۡمُطَّوِّعِينَ مِنَ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ فِي ٱلصَّدَقَٰتِ وَٱلَّذِينَ لَا يَجِدُونَ إِلَّا جُهۡدَهُمۡ فَيَسۡخَرُونَ مِنۡهُمۡ سَخِرَ ٱللَّهُ مِنۡهُمۡ وَلَهُمۡ عَذَابٌ أَلِيمٌ ﴾
[التوبَة: 79]

Iwo amene amaononga mbiri ya anthu okhulupirira amene amapereka mosaumilizidwa ndi iwo amene sanapeza chopereka kupatula chimene ali nacho, motero iwo amanyoza. Mulungu adzawabwezera mtozo wawo. Motero chawo chidzakhala chilango chowawa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الذين يلمزون المطوعين من المؤمنين في الصدقات والذين لا يجدون إلا جهدهم, باللغة نيانجا

﴿الذين يلمزون المطوعين من المؤمنين في الصدقات والذين لا يجدون إلا جهدهم﴾ [التوبَة: 79]

Khaled Ibrahim Betala
“Amene akuwanyogodola okhulupirira opereka sadaka yambiri, ndiponso (amene akunyoza) amene sapeza (chopereka) koma chinthu chochepa; ndikumawachitira chipongwe, Allah adzawalipira chipongwe chawocho. Iwo adzapeza chilango chopweteka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek