Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 81 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿فَرِحَ ٱلۡمُخَلَّفُونَ بِمَقۡعَدِهِمۡ خِلَٰفَ رَسُولِ ٱللَّهِ وَكَرِهُوٓاْ أَن يُجَٰهِدُواْ بِأَمۡوَٰلِهِمۡ وَأَنفُسِهِمۡ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِ وَقَالُواْ لَا تَنفِرُواْ فِي ٱلۡحَرِّۗ قُلۡ نَارُ جَهَنَّمَ أَشَدُّ حَرّٗاۚ لَّوۡ كَانُواْ يَفۡقَهُونَ ﴾
[التوبَة: 81]
﴿فرح المخلفون بمقعدهم خلاف رسول الله وكرهوا أن يجاهدوا بأموالهم وأنفسهم في﴾ [التوبَة: 81]
Khaled Ibrahim Betala “Akondwa amene adasiidwa m’mbuyo (osapita kunkhondo) chifukwa chakukhala kwawo m’mbuyo polekana ndi Mtumiki wa Allah, nakuda kumenyana pa njira ya Allah ndi chuma chawo ndi miyoyo yawo, nati (kwa anzawo): “Musapite (ku nkhondo) m’nthawi yotenthayi.” Auze: “Moto wa Jahannam ngotentha kwambiri akadakhala akuzindikira.” |