Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 87 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿رَضُواْ بِأَن يَكُونُواْ مَعَ ٱلۡخَوَالِفِ وَطُبِعَ عَلَىٰ قُلُوبِهِمۡ فَهُمۡ لَا يَفۡقَهُونَ ﴾
[التوبَة: 87]
﴿رضوا بأن يكونوا مع الخوالف وطبع على قلوبهم فهم لا يفقهون﴾ [التوبَة: 87]
Khaled Ibrahim Betala “Akondwera pokhala limodzi ndi otsalira m’mbuyo (akazi ndi ana). Ndipo mitima yawo yadindidwa chidindo (yatsekedwa), choncho iwo sazindikira |