Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 88 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿لَٰكِنِ ٱلرَّسُولُ وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ مَعَهُۥ جَٰهَدُواْ بِأَمۡوَٰلِهِمۡ وَأَنفُسِهِمۡۚ وَأُوْلَٰٓئِكَ لَهُمُ ٱلۡخَيۡرَٰتُۖ وَأُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلۡمُفۡلِحُونَ ﴾
[التوبَة: 88]
﴿لكن الرسول والذين آمنوا معه جاهدوا بأموالهم وأنفسهم وأولئك لهم الخيرات وأولئك﴾ [التوبَة: 88]
Khaled Ibrahim Betala “Koma Mtumiki ndi amene akhulupirira pamodzi ndi iye amenya nkhondo ndi chuma chawo ndi matupi awo. Iwowo ndiwo opeza zabwino, ndiponso iwowo ndiwo opambana |