Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 95 - التوبَة - Page - Juz 11
﴿سَيَحۡلِفُونَ بِٱللَّهِ لَكُمۡ إِذَا ٱنقَلَبۡتُمۡ إِلَيۡهِمۡ لِتُعۡرِضُواْ عَنۡهُمۡۖ فَأَعۡرِضُواْ عَنۡهُمۡۖ إِنَّهُمۡ رِجۡسٞۖ وَمَأۡوَىٰهُمۡ جَهَنَّمُ جَزَآءَۢ بِمَا كَانُواْ يَكۡسِبُونَ ﴾
[التوبَة: 95]
﴿سيحلفون بالله لكم إذا انقلبتم إليهم لتعرضوا عنهم فأعرضوا عنهم إنهم رجس﴾ [التوبَة: 95]
Khaled Ibrahim Betala “Mukabwerera kwa iwo, adzalumbira m’dzina la Allah kwa inu kuti muwasiye (musawachite kanthu). Choncho, apatukireni. Ndithu iwo ndiuve ndipo malo awo ndi ku Jahannam. Iyi ndi mphoto ya zomwe adali kupeza (kuchokera m’zochita zawo zoipa) |