Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 105 - يُونس - Page - Juz 11
﴿وَأَنۡ أَقِمۡ وَجۡهَكَ لِلدِّينِ حَنِيفٗا وَلَا تَكُونَنَّ مِنَ ٱلۡمُشۡرِكِينَ ﴾
[يُونس: 105]
﴿وأن أقم وجهك للدين حنيفا ولا تكونن من المشركين﴾ [يُونس: 105]
Khaled Ibrahim Betala ““Ndiponso (ndauzidwa kuti): ‘Lungamitsa nkhope yako kuchipembedzo momuyeretsera Allah mapemphero Ake, ndipo usakhale mmodzi mwa ophatikiza (Allah ndi zinthu zina).’ |