Quran with Chichewa translation - Surah Hud ayat 55 - هُود - Page - Juz 12
﴿مِن دُونِهِۦۖ فَكِيدُونِي جَمِيعٗا ثُمَّ لَا تُنظِرُونِ ﴾
[هُود: 55]
﴿من دونه فكيدوني جميعا ثم لا تنظرون﴾ [هُود: 55]
Khaled Ibrahim Betala ““Kusiya Iye; (milungu yanuyo sindikuiopa ngati ili ndi mphamvu pamodzi ndi inu), tero ndichitireni chiwembu nonsenu, ndipo kenako musandiyembekezere (musandipatse nthawi).” |