Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 20 - يُوسُف - Page - Juz 12
﴿وَشَرَوۡهُ بِثَمَنِۭ بَخۡسٖ دَرَٰهِمَ مَعۡدُودَةٖ وَكَانُواْ فِيهِ مِنَ ٱلزَّٰهِدِينَ ﴾
[يُوسُف: 20]
﴿وشروه بثمن بخس دراهم معدودة وكانوا فيه من الزاهدين﴾ [يُوسُف: 20]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adamgulitsa pa mtengo wochepa ndi ndalama zapang’ono, zowerengeka (poopa kuti angawadzere eni mwanayo). Ndipo sadalabadire za iye |