×

Ndipo pamene mthenga wa nkhani zabwino adadza iye adaponya malaya a Yosefe 12:96 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yusuf ⮕ (12:96) ayat 96 in Chichewa

12:96 Surah Yusuf ayat 96 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yusuf ayat 96 - يُوسُف - Page - Juz 13

﴿فَلَمَّآ أَن جَآءَ ٱلۡبَشِيرُ أَلۡقَىٰهُ عَلَىٰ وَجۡهِهِۦ فَٱرۡتَدَّ بَصِيرٗاۖ قَالَ أَلَمۡ أَقُل لَّكُمۡ إِنِّيٓ أَعۡلَمُ مِنَ ٱللَّهِ مَا لَا تَعۡلَمُونَ ﴾
[يُوسُف: 96]

Ndipo pamene mthenga wa nkhani zabwino adadza iye adaponya malaya a Yosefe pamaso pake, ndipo nthawi yomweyo adayambanso kupenya. Iye adati, “Kodi ine sindidakuuzeni kuti ine ndinali kudziwa, kuchokera kwa Mulungu, zinthu zimene inu simuzidziwa?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فلما أن جاء البشير ألقاه على وجهه فارتد بصيرا قال ألم أقل, باللغة نيانجا

﴿فلما أن جاء البشير ألقاه على وجهه فارتد بصيرا قال ألم أقل﴾ [يُوسُف: 96]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho pamene adadza wotenga nkhani yabwino, adauponya (mkanjo wa Yûsuf) pankhope pake, ndipo pompo adapenya. Adati: “Kodi sindinakuuzeni kuti ine ndikudziwa kupyolera mwa Allah zomwe inu simukuzidziwa?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek