Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 1 - الرَّعد - Page - Juz 13
﴿الٓمٓرۚ تِلۡكَ ءَايَٰتُ ٱلۡكِتَٰبِۗ وَٱلَّذِيٓ أُنزِلَ إِلَيۡكَ مِن رَّبِّكَ ٱلۡحَقُّ وَلَٰكِنَّ أَكۡثَرَ ٱلنَّاسِ لَا يُؤۡمِنُونَ ﴾
[الرَّعد: 1]
﴿المر تلك آيات الكتاب والذي أنـزل إليك من ربك الحق ولكن أكثر﴾ [الرَّعد: 1]
Khaled Ibrahim Betala “Alif-Lâm-Mîm-Râ. Izi ndi Ayah (ndime) za buku ili (lomwe lasonkhanitsa chilichonse chofunika); ndipo chomwe chavumbulutsidwa kwa iwe kuchokera kwa Mbuye wako, nchoonadi; koma anthu ambiri sakhulupirira |