Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 10 - الرَّعد - Page - Juz 13
﴿سَوَآءٞ مِّنكُم مَّنۡ أَسَرَّ ٱلۡقَوۡلَ وَمَن جَهَرَ بِهِۦ وَمَنۡ هُوَ مُسۡتَخۡفِۭ بِٱلَّيۡلِ وَسَارِبُۢ بِٱلنَّهَارِ ﴾
[الرَّعد: 10]
﴿سواء منكم من أسر القول ومن جهر به ومن هو مستخف بالليل﴾ [الرَّعد: 10]
Khaled Ibrahim Betala “Ndi chimodzimodzi (kwa Iye Allah) amene akubisa liwu lake mwa inu ndi amene akulikweza ndi yemwe akudzibisa usiku ndi yemwe akuyenda usana, (onse akuwadziwa) |