Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 21 - الرَّعد - Page - Juz 13
﴿وَٱلَّذِينَ يَصِلُونَ مَآ أَمَرَ ٱللَّهُ بِهِۦٓ أَن يُوصَلَ وَيَخۡشَوۡنَ رَبَّهُمۡ وَيَخَافُونَ سُوٓءَ ٱلۡحِسَابِ ﴾
[الرَّعد: 21]
﴿والذين يصلون ما أمر الله به أن يوصل ويخشون ربهم ويخافون سوء﴾ [الرَّعد: 21]
Khaled Ibrahim Betala “Ndiponso omwe akulumikiza zomwe Allah walamula kuti zilumikizidwe (monga chibale), pamodzi ndi kuopa Mbuye wawo ndi kuopanso chiwerengero choipa (chomwe chidzawapeza oipa tsiku lachimaliziro tero amayesetsa kuwapatuka machitidwe oipa) |