×

Ndipo ndithudi Atumwi ambiri adanyozedwa iwe usanadze ndipo Ine ndidawalekerera anthu osakhulupirira, 13:32 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ar-Ra‘d ⮕ (13:32) ayat 32 in Chichewa

13:32 Surah Ar-Ra‘d ayat 32 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Ra‘d ayat 32 - الرَّعد - Page - Juz 13

﴿وَلَقَدِ ٱسۡتُهۡزِئَ بِرُسُلٖ مِّن قَبۡلِكَ فَأَمۡلَيۡتُ لِلَّذِينَ كَفَرُواْ ثُمَّ أَخَذۡتُهُمۡۖ فَكَيۡفَ كَانَ عِقَابِ ﴾
[الرَّعد: 32]

Ndipo ndithudi Atumwi ambiri adanyozedwa iwe usanadze ndipo Ine ndidawalekerera anthu osakhulupirira, ndipo pomaliza ndidawalanga. Kodi chilango changa chidali chowawa bwanji

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد استهزئ برسل من قبلك فأمليت للذين كفروا ثم أخذتهم فكيف كان, باللغة نيانجا

﴿ولقد استهزئ برسل من قبلك فأمليت للذين كفروا ثم أخذتهم فكيف كان﴾ [الرَّعد: 32]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu adachitidwa chipongwe atumiki akale iwe usanadze koma ndidawalekelera amene sadakhulupirire (sindidawalange mwachangu), ndipo kenako ndidawalanga. Kodi chilango changa chidali chotani
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek