×

“Kodi ife tingalekerenji kuika chikhulupiriro chathu mwa Mulungu pamene Iye watitsogolera kunjira 14:12 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ibrahim ⮕ (14:12) ayat 12 in Chichewa

14:12 Surah Ibrahim ayat 12 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ibrahim ayat 12 - إبراهِيم - Page - Juz 13

﴿وَمَا لَنَآ أَلَّا نَتَوَكَّلَ عَلَى ٱللَّهِ وَقَدۡ هَدَىٰنَا سُبُلَنَاۚ وَلَنَصۡبِرَنَّ عَلَىٰ مَآ ءَاذَيۡتُمُونَاۚ وَعَلَى ٱللَّهِ فَلۡيَتَوَكَّلِ ٱلۡمُتَوَكِّلُونَ ﴾
[إبراهِيم: 12]

“Kodi ife tingalekerenji kuika chikhulupiriro chathu mwa Mulungu pamene Iye watitsogolera kunjira zathu? Ndithudi ife tidzapirira ku mazunzo amene mungatipatse ife ndipo mwa Mulungu, onse amene amakhulupirira aike chikhulupiriro chawo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما لنا ألا نتوكل على الله وقد هدانا سبلنا ولنصبرن على ما, باللغة نيانجا

﴿وما لنا ألا نتوكل على الله وقد هدانا سبلنا ولنصبرن على ما﴾ [إبراهِيم: 12]

Khaled Ibrahim Betala
““Nanga kwa ife kuli chiyani kuti tisatsamire kwa Allah pomwe watisonyeza njira zathu. Ndipo tipirira pa zimene mukutisautsa nazo. Choncho, kwa Allah Yekha atsamire otsamira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek