×

Ife timadziwa kwambiri zimene iwo akumva ndi pamene amamvetsera kwa iwe. Ndipo 17:47 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:47) ayat 47 in Chichewa

17:47 Surah Al-Isra’ ayat 47 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 47 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿نَّحۡنُ أَعۡلَمُ بِمَا يَسۡتَمِعُونَ بِهِۦٓ إِذۡ يَسۡتَمِعُونَ إِلَيۡكَ وَإِذۡ هُمۡ نَجۡوَىٰٓ إِذۡ يَقُولُ ٱلظَّٰلِمُونَ إِن تَتَّبِعُونَ إِلَّا رَجُلٗا مَّسۡحُورًا ﴾
[الإسرَاء: 47]

Ife timadziwa kwambiri zimene iwo akumva ndi pamene amamvetsera kwa iwe. Ndipo pamene amanong’onezana, taona anthu oipa, amanena kuti: “Inu mukutsatira munthu wolodzedwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: نحن أعلم بما يستمعون به إذ يستمعون إليك وإذ هم نجوى إذ, باللغة نيانجا

﴿نحن أعلم بما يستمعون به إذ يستمعون إليك وإذ هم نجوى إذ﴾ [الإسرَاء: 47]

Khaled Ibrahim Betala
“Ife tikudziwa chifukwa chomwe akuimvetsera (Qur’an), pamene akukumvetsera ndi pamene akunong’onezana awo achinyengo, pamene akunena awo oyipa (kuuza Asilamu kuti): “Inu simutsatira (wina) koma munthu wolodzedwa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek