×

Ndipo palibe chimene chimatiletsa Ife kutumiza zizindikiro kupatula kuti anthu a mvula 17:59 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Isra’ ⮕ (17:59) ayat 59 in Chichewa

17:59 Surah Al-Isra’ ayat 59 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Isra’ ayat 59 - الإسرَاء - Page - Juz 15

﴿وَمَا مَنَعَنَآ أَن نُّرۡسِلَ بِٱلۡأٓيَٰتِ إِلَّآ أَن كَذَّبَ بِهَا ٱلۡأَوَّلُونَۚ وَءَاتَيۡنَا ثَمُودَ ٱلنَّاقَةَ مُبۡصِرَةٗ فَظَلَمُواْ بِهَاۚ وَمَا نُرۡسِلُ بِٱلۡأٓيَٰتِ إِلَّا تَخۡوِيفٗا ﴾
[الإسرَاء: 59]

Ndipo palibe chimene chimatiletsa Ife kutumiza zizindikiro kupatula kuti anthu a mvula zakale sadazikhulupirire izo. Ndipo kwa anthu a Thamoud, Ife tidawapatsa ngamira yaikazi kukhala chizindikiro chooneka ndi maso komabe iwo adaichitira zoipa. Ndipo Ife sititumiza zizindikiro kupatula ndi cholinga chofuna kuchenjeza ndi kuwachititsa mantha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما منعنا أن نرسل بالآيات إلا أن كذب بها الأولون وآتينا ثمود, باللغة نيانجا

﴿وما منعنا أن نرسل بالآيات إلا أن كذب بها الأولون وآتينا ثمود﴾ [الإسرَاء: 59]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo palibe chimene chikutiletsa kutumiza zizizwa (zomwe akuzipempha) koma kuti anthu akale adazitsutsa. Asamuda tidawapatsa ngamira yaikazi kuti ikhale chizindikiro choonekera (chozizwitsa) koma adaichitira zosayenera; ndipo sititumiza zizizwa ndi cholinga china, koma kuchenjeza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek