Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 77 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿أَفَرَءَيۡتَ ٱلَّذِي كَفَرَ بِـَٔايَٰتِنَا وَقَالَ لَأُوتَيَنَّ مَالٗا وَوَلَدًا ﴾
[مَريَم: 77]
﴿أفرأيت الذي كفر بآياتنا وقال لأوتين مالا وولدا﴾ [مَريَم: 77]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi wamuona yemwe watsutsa Ayah Zathu ndikunena kuti: “Ndithu ndidzapatsidwa chuma ndi ana (pa tsiku lachimaliziro monga momwe andipatsira pano pa dziko?)” |