×

Kodi iye waziona zinthu zosaoneka kapena Mwini chisoni chosatha wamupatsa lonjezo lotere 19:78 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Maryam ⮕ (19:78) ayat 78 in Chichewa

19:78 Surah Maryam ayat 78 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 78 - مَريَم - Page - Juz 16

﴿أَطَّلَعَ ٱلۡغَيۡبَ أَمِ ٱتَّخَذَ عِندَ ٱلرَّحۡمَٰنِ عَهۡدٗا ﴾
[مَريَم: 78]

Kodi iye waziona zinthu zosaoneka kapena Mwini chisoni chosatha wamupatsa lonjezo lotere

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أطلع الغيب أم اتخذ عند الرحمن عهدا, باللغة نيانجا

﴿أطلع الغيب أم اتخذ عند الرحمن عهدا﴾ [مَريَم: 78]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi adadziwa zamseri, kapena adalandira lonjezo kwa Allah mwini chifundo Chambiri (kotero kuti ali ndi chikhulupiliro pa zimene akunenazo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek