Quran with Chichewa translation - Surah Maryam ayat 84 - مَريَم - Page - Juz 16
﴿فَلَا تَعۡجَلۡ عَلَيۡهِمۡۖ إِنَّمَا نَعُدُّ لَهُمۡ عَدّٗا ﴾
[مَريَم: 84]
﴿فلا تعجل عليهم إنما نعد لهم عدا﴾ [مَريَم: 84]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho, usawachitire changu (kuti alangidwe tsopano), ndithu Ife tikuwawerengera chiwerengero (cha masiku awo; masiku akakwana, tiwalanga) |