×

Ndipo iwo amene akufa ndi kusiya akazi, akaziwo ayenera kudikira, osakwatiwa miyezi 2:234 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Baqarah ⮕ (2:234) ayat 234 in Chichewa

2:234 Surah Al-Baqarah ayat 234 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Baqarah ayat 234 - البَقَرَة - Page - Juz 2

﴿وَٱلَّذِينَ يُتَوَفَّوۡنَ مِنكُمۡ وَيَذَرُونَ أَزۡوَٰجٗا يَتَرَبَّصۡنَ بِأَنفُسِهِنَّ أَرۡبَعَةَ أَشۡهُرٖ وَعَشۡرٗاۖ فَإِذَا بَلَغۡنَ أَجَلَهُنَّ فَلَا جُنَاحَ عَلَيۡكُمۡ فِيمَا فَعَلۡنَ فِيٓ أَنفُسِهِنَّ بِٱلۡمَعۡرُوفِۗ وَٱللَّهُ بِمَا تَعۡمَلُونَ خَبِيرٞ ﴾
[البَقَرَة: 234]

Ndipo iwo amene akufa ndi kusiya akazi, akaziwo ayenera kudikira, osakwatiwa miyezi inayi ndi masiku khumi, ndipo iwo akakwaniritsa nthawi iyi, inu simudzakhala ndi mlandu pa zimene iwo achita molingana ndi malamulo. Ndipo Mulungu amadziwa zonse zimene mumachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين يتوفون منكم ويذرون أزواجا يتربصن بأنفسهن أربعة أشهر وعشرا فإذا بلغن, باللغة نيانجا

﴿والذين يتوفون منكم ويذرون أزواجا يتربصن بأنفسهن أربعة أشهر وعشرا فإذا بلغن﴾ [البَقَرَة: 234]

Khaled Ibrahim Betala
Ndipo mwa inu amene amwalira nasiya akazi, choncho (akaziwo) ayembekezere (asakwatiwe) miyezi inayi ndi masiku khumi. Ndipo akakwanitsa nyengo ya chiyembekezero chawo cha edda, sitchimo kwa inu pazimene akaziwo adzichitira okha (monga kudzikongoletsa ndi kudziwonetsa kwa ofunsira ukwati); motsatira malamulo a Shariya. Ndipo Allah Ngodziwa zonse zimene mukuchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek