×

Iye adati, “Iyayi. Ponyani zanu poyamba.” Ndipo taona ndi mphamvu ya matsenga 20:66 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ta-Ha ⮕ (20:66) ayat 66 in Chichewa

20:66 Surah Ta-Ha ayat 66 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 66 - طه - Page - Juz 16

﴿قَالَ بَلۡ أَلۡقُواْۖ فَإِذَا حِبَالُهُمۡ وَعِصِيُّهُمۡ يُخَيَّلُ إِلَيۡهِ مِن سِحۡرِهِمۡ أَنَّهَا تَسۡعَىٰ ﴾
[طه: 66]

Iye adati, “Iyayi. Ponyani zanu poyamba.” Ndipo taona ndi mphamvu ya matsenga awo, zingwe ndi ndodo zawo zidaoneka, m’maso mwa Mose, kuti zinali kuyenda mofulumira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال بل ألقوا فإذا حبالهم وعصيهم يخيل إليه من سحرهم أنها تسعى, باللغة نيانجا

﴿قال بل ألقوا فإذا حبالهم وعصيهم يخيل إليه من سحرهم أنها تسعى﴾ [طه: 66]

Khaled Ibrahim Betala
“(Mûsa) adati: “Koma inu ndinu muponye!” (Choncho adaponya matsengawo). Mwadzidzidzi zingwe zawo ndi ndodo zawo zamatsenga awo, zimaoneka pamaso pake (Mûsa) kuti zikuyenda mothamanga
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek