×

Akadakhala kuti anthu osakhulupirira akudziwa tsiku limene iwo sadzakhala ndi mphamvu zophimba 21:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anbiya’ ⮕ (21:39) ayat 39 in Chichewa

21:39 Surah Al-Anbiya’ ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 39 - الأنبيَاء - Page - Juz 17

﴿لَوۡ يَعۡلَمُ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ حِينَ لَا يَكُفُّونَ عَن وُجُوهِهِمُ ٱلنَّارَ وَلَا عَن ظُهُورِهِمۡ وَلَا هُمۡ يُنصَرُونَ ﴾
[الأنبيَاء: 39]

Akadakhala kuti anthu osakhulupirira akudziwa tsiku limene iwo sadzakhala ndi mphamvu zophimba nkhope kapena misana yawo kudziteteza ku moto ndipo iwo sangathandizike

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لو يعلم الذين كفروا حين لا يكفون عن وجوههم النار ولا عن, باللغة نيانجا

﴿لو يعلم الذين كفروا حين لا يكفون عن وجوههم النار ولا عن﴾ [الأنبيَاء: 39]

Khaled Ibrahim Betala
“Chikhala kuti amene sadakhulupirire akudziwa chilango chimene chidzawapeza panthawi yomwe sangathe kutchinjiriza Moto kunkhope zawo ndi kumisana yawo ndipo kuti sadzathandizidwa, (sakadanena zimenezi)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek