Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 12 - الحج - Page - Juz 17
﴿يَدۡعُواْ مِن دُونِ ٱللَّهِ مَا لَا يَضُرُّهُۥ وَمَا لَا يَنفَعُهُۥۚ ذَٰلِكَ هُوَ ٱلضَّلَٰلُ ٱلۡبَعِيدُ ﴾
[الحج: 12]
﴿يدعو من دون الله ما لا يضره وما لا ينفعه ذلك هو﴾ [الحج: 12]
Khaled Ibrahim Betala “M’malo mwa Allah, amapembedza zomwe sizingampatse masautso (ngati ataleka kuzipembedza), ndiponso zomwe sizingampatse chithandizo (akamazipembedza), ndipo kumeneko ndiko kusokera konka nako kutali |