×

Ndithudi Mulungu adzawalowetsa onse amene amakhulupilira ndipo amachita ntchito zabwino m’minda yothiriridwa 22:14 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hajj ⮕ (22:14) ayat 14 in Chichewa

22:14 Surah Al-hajj ayat 14 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 14 - الحج - Page - Juz 17

﴿إِنَّ ٱللَّهَ يُدۡخِلُ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ جَنَّٰتٖ تَجۡرِي مِن تَحۡتِهَا ٱلۡأَنۡهَٰرُۚ إِنَّ ٱللَّهَ يَفۡعَلُ مَا يُرِيدُ ﴾
[الحج: 14]

Ndithudi Mulungu adzawalowetsa onse amene amakhulupilira ndipo amachita ntchito zabwino m’minda yothiriridwa ndi mitsinje ndi madzi oyenda. Ndithudi Mulungu amachita zimene afuna

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الله يدخل الذين آمنوا وعملوا الصالحات جنات تجري من تحتها الأنهار, باللغة نيانجا

﴿إن الله يدخل الذين آمنوا وعملوا الصالحات جنات تجري من تحتها الأنهار﴾ [الحج: 14]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Allah adzawalowetsa ku Minda yamtendere amene akhulupirira ndikuchita zabwino, mitsinje ikuyenda pansi (pa mindayo). Ndithu Allah amachita chimene wafuna
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek