Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 76 - الحج - Page - Juz 17
﴿يَعۡلَمُ مَا بَيۡنَ أَيۡدِيهِمۡ وَمَا خَلۡفَهُمۡۚ وَإِلَى ٱللَّهِ تُرۡجَعُ ٱلۡأُمُورُ ﴾
[الحج: 76]
﴿يعلم ما بين أيديهم وما خلفهم وإلى الله ترجع الأمور﴾ [الحج: 76]
Khaled Ibrahim Betala “Akudziwa zimene zili patsogolo pawo ndi zimene zili pambuyo pawo; kwa Allah Yekha ndiko kobwerera zinthu |