Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 107 - المؤمنُون - Page - Juz 18
﴿رَبَّنَآ أَخۡرِجۡنَا مِنۡهَا فَإِنۡ عُدۡنَا فَإِنَّا ظَٰلِمُونَ ﴾
[المؤمنُون: 107]
﴿ربنا أخرجنا منها فإن عدنا فإنا ظالمون﴾ [المؤمنُون: 107]
Khaled Ibrahim Betala “Mbuye wathu! Titulutseni umu (m’moto ndikutibwezera ku dziko lapansi kuti tikachite ntchito yabwino); ngati titabwerezanso kuchita zoipa, ndiye kuti tidzakhaladi oipa (odziononga tokha).” |