Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 88 - المؤمنُون - Page - Juz 18
﴿قُلۡ مَنۢ بِيَدِهِۦ مَلَكُوتُ كُلِّ شَيۡءٖ وَهُوَ يُجِيرُ وَلَا يُجَارُ عَلَيۡهِ إِن كُنتُمۡ تَعۡلَمُونَ ﴾
[المؤمنُون: 88]
﴿قل من بيده ملكوت كل شيء وهو يجير ولا يجار عليه إن﴾ [المؤمنُون: 88]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Kodi ndani yemwe m’manja mwake muli mphamvu yolamulira chinthu chilichonse? Ndipo Iye amateteza zonse. Ndipo palibe chimene chingatetezedwe kuchilango Chake. Ngati inu mukudziwa.” |