Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 28 - النور - Page - Juz 18
﴿فَإِن لَّمۡ تَجِدُواْ فِيهَآ أَحَدٗا فَلَا تَدۡخُلُوهَا حَتَّىٰ يُؤۡذَنَ لَكُمۡۖ وَإِن قِيلَ لَكُمُ ٱرۡجِعُواْ فَٱرۡجِعُواْۖ هُوَ أَزۡكَىٰ لَكُمۡۚ وَٱللَّهُ بِمَا تَعۡمَلُونَ عَلِيمٞ ﴾
[النور: 28]
﴿فإن لم تجدوا فيها أحدا فلا تدخلوها حتى يؤذن لكم وإن قيل﴾ [النور: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Koma ngati simupeza munthu aliyense m’menemo, musalowe kufikira mutapatsidwa chilolezo. Ndipo mukauzidwa kuti: “Bwererani.” Bwererani; chimenechi nchokuyeretsani. Ndipo Allah akudziwa zimene muchita |