×

Sichidzakhala cholakwa ngati inu mulowa m’nyumba zopanda okhalamo zomwe muli nazo ndi 24:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:29) ayat 29 in Chichewa

24:29 Surah An-Nur ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 29 - النور - Page - Juz 18

﴿لَّيۡسَ عَلَيۡكُمۡ جُنَاحٌ أَن تَدۡخُلُواْ بُيُوتًا غَيۡرَ مَسۡكُونَةٖ فِيهَا مَتَٰعٞ لَّكُمۡۚ وَٱللَّهُ يَعۡلَمُ مَا تُبۡدُونَ وَمَا تَكۡتُمُونَ ﴾
[النور: 29]

Sichidzakhala cholakwa ngati inu mulowa m’nyumba zopanda okhalamo zomwe muli nazo ndi ntchito. Mulungu amadziwa zonse zimene mumaulula ndi zimene mumabista

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ليس عليكم جناح أن تدخلوا بيوتا غير مسكونة فيها متاع لكم والله, باللغة نيانجا

﴿ليس عليكم جناح أن تدخلوا بيوتا غير مسكونة فيها متاع لكم والله﴾ [النور: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Sikulakwa kwa inu kulowa m’nyumba zosakhalidwa, (monga sitolo, hotela; popanda chilolezo), momwe muli zokuthandizani; ndipo Allah akudziwa zomwe mukuonetsera poyera ndi zimene mukubisa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek