×

Ife takutumizirani inu chivumbulutso chooneka bwino ndipo takupatsani chitsanzo cha anthu amene 24:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:34) ayat 34 in Chichewa

24:34 Surah An-Nur ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 34 - النور - Page - Juz 18

﴿وَلَقَدۡ أَنزَلۡنَآ إِلَيۡكُمۡ ءَايَٰتٖ مُّبَيِّنَٰتٖ وَمَثَلٗا مِّنَ ٱلَّذِينَ خَلَوۡاْ مِن قَبۡلِكُمۡ وَمَوۡعِظَةٗ لِّلۡمُتَّقِينَ ﴾
[النور: 34]

Ife takutumizirani inu chivumbulutso chooneka bwino ndipo takupatsani chitsanzo cha anthu amene adalipo kale ndi chilangizo kwa anthu angwiro

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد أنـزلنا إليكم آيات مبينات ومثلا من الذين خلوا من قبلكم وموعظة, باللغة نيانجا

﴿ولقد أنـزلنا إليكم آيات مبينات ومثلا من الذين خلوا من قبلكم وموعظة﴾ [النور: 34]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu tatumiza kwa inu Ayah (ndime) zofotokoza (zofunika zonse) mwatsatanetsatane, ndi mafanizo (okuphanulani maso) pa za amene adamuka patsogolo panu, ndi phunziro kwa oopa (Allah)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek